
6 July ili ku BNS
Nduna ya zofalitsa nkhani a Moses Kunkuyu apempha Amalawi amene akudzapita ku chisangalalo choti dziko lino lakwanitsa zaka 61 lili pa ufulu wodzilamulira kuti adzapewe kutenga zakumwa zoledzeretsa ngakhalenso kunyamula zida popita ku mwambowu ku Bingu …